
Student/Hustle ✌️/ silver strikes 🩵and Matchester united ♥️ HONCHO 🫰 @graysamson754@gmail.com
Malawi
Joined January 2025
- Tweets2.2K
- Following842
- Followers426
- Likes2.6K
GRAY★ retweeted
PLEASE LET'S HELP CATHERINE WITH ANY LITTLE AMOUNT THAT WE HAVE.🙏
Dzina langa ndi Catherine Kawerere, ndili ndi zaka 22, ndimakhala ku Kasungu.
Kuyambira 2019 ndili ndi vuto la impsyo (kidneys). Tsopano madokotala akuti ndikufunika Kidney Transplant ku India mwachangu.
Wopereka Kidney wapezeka kale, koma ndikufunika *K46 Million* kuti ulendowu utheke. Makolo anga alibe kuthekera.
Sabata iliyonse ndimafunika ndipita ku Kamuzu Central Hospital kawiri ku Dialysis.
Chonde ndithandizeni, ngakhale kugawana uthengawu.
Kulumikizana:
0995759754 - Catherine
0999635902 - Masauko Kawerere
0996761010 / 0999641497 - Getrude Nthukwa
Bank:
Standard Bank: 10003020336
Acc Name: Masauko Kawerere
RT for awareness.🙏❤️
GRAY★ retweeted
Chinayamba kugwira ndalama kalekale ! 🙌🏾
Zosadabwitsa chikumagawa ndalama ma show, moti ku Concert yakeyi 'Tigona Panja ' pa 31 Zezember chayenera chigawaso ma cash !
Ma ticket ndiye paja a 10K ndi 20K akutha mwezi uno wa October.
Apa zikungofunika kuguliratu asanadhule, kuti akamakagawa zakezo ukaomboleko yako !
Momwe mungapezere ma ticket 👇🏾
GRAY★ retweeted
🚨 OFFICIAL: Lisandro Martínez releases new statement after meeting with Carrick and club directors.
“Today I met with the club’s leadership and the manager. It was a very positive conversation, where we were able to exchange views and speak openly about what happened after the game”.
“Everyone knows that I am a passionate person and that I live football with great intensity. The frustration of the defeat led me to express how I felt at a time and place that perhaps were not the right ones, and for that I want to apologise”.
“Our club is at its best when we are all united, and I recognise that my words in that moment did not help with that”.
“I know that every single person at Manchester United is doing everything possible to achieve our shared ambition: bringing the success that this club and its supporters deserve”.
“With this situation now behind us, we are fully focused on winning together”.































