Enanu vuto umphawi umakusangalasani ndiye tikapereka nzeru pano simumva. Mnyamata uyu ali pa Khameli akufuna aliyese azipezako kanganyase pakutha patsiku ndiye akumavumbitsa ma live uku mkumagawa mtonyo. Ndiye poti umphawi unakupolamirani mupezeka iziso zakuphonyani. 🔨
linkie : Kick.com/rayhan265
115
Alandire ulemu wake Admore Chiumia 🔥
Admore Chiumia has made history by becoming the first PhD candidate to successfully defend his doctoral thesis at the Malawi University of Business and Applied Sciences (MUBAS) since the institution’s delinking from the University of Malawi in 2021.
If you know him tag him timuyamikire mwapadera 🤝
2
177
Dolo kwambiri. Mwisho Mhango osawela pakati wa team ya Hannover 96 ku Germany komanso Malawi National Team.
Akachita mwayi team yake itha kulowa mu Bundesliga ma season akubwerawa azikaphana phana ndi achina Harry Kane, Olise ndi ena ambiri.
Source: German Embassy Lilongwe
1
5
326
Changowona kukhala chakuda koma chili ndi mtima wabho komaso khalidwe la Nyatwa
Last weekend Gwamba anali ku Phalombe, Nchalo and Nsanje komwe anapereka mwai kwa ma upc and coming artists okwana 15 kuti apange perform. Mwa anthu onsewo munthu amene anabwera kuzathokoza anali uyu Tesyn waku Nsanje basi.
Nde tufuna mutenge nthawi yanu yochepa chabe mukaone Luso lake lomwe ali nalo, ena aphunzirepo kuti khalidwe ndi chuma.
Linkie: comment section.
2
398
Zani Challe wakanilatu ati zisamukhudze iyeyo sali ku Nigeria ali ku Japan. Kwavutilatu ku Nigeria
287
Iyi ndi list ya azimayi aluso aku Malawi omwe apita ku Nigeria:
1. Taurai Mache Yvonne
2. Xandria
3. Theresa Phondo
4. Dorothy Kingston
5. Temwah
Bonus List
Azimayi aluso omwe ali madera ena osati Nigeria:
Lady Aika aliku China
Zani Challe ali ku Japan
Queen Mishu ali ku South Africa
Sife ali ku Dubai waku 49
1
10
2,005
Mega Magnate ati anakhala zaka 4 osagonana ndi munthu aliyense chifukwa chofuna kuika maganizo ake pa zolinga zake! Akulangiza anyamata kuti azitha kudziletsa pa nkhani ya sex komanso kuika patsogolo tsogolo lawo. Khalani ndi chilakolako, koma musaiwale zolinga zanu!
2
268
Happy Heavenly Birthday, ECL! A leader whose name remains etched in Zambia’s history. Gone but never forgotten. Continue resting in peace, Edgar Chagwa Lungu.
Apa ndi pamene umadziwira kuti udolo wa Wendy Favour Harawa siogwera chabe. Zina mwa nyimbo zake ndi izi:
Gospel Songs
1. Mundisunge Ndinu
2. M’busa Wanga
3. Hossana
4. Ameneyu Ndani
5. I Believe (feat. Lulu)
6. Zikomo (feat. Levixone)
7. Tiyamike
8. Papa Love
9. Mulamulire (feat. Kondwani Chirwa)
10. Favour
11. Over and Over
12. Chisomo (feat. Jimmy D Psalmist & Lulu)
13. Ambuye Ndionetseni
14. Obikyusiza (feat. Colifixe)
15. Kuhambelela (feat. Maranatha Goroh)
16. Hallelujah (feat. Abel Chungu)
SECULAR SONGS
1. Ndakana
2. Unalonjeza
3. Sindirichoncho (feat. Lulu)
4. Wandidolola (feat. Lucius Banda)
5. Okondedwa Wanga (feat. Lucius Banda)
6. Chotselen Mkwiyo
7. Silira
8. Akuwona (feat. Guardian Angel)
9. Tigwilane Manja (feat. Lulu, Lucius Banda & Skeffa Chimoto)
10. Moto
11. Praise Your Name
Note: This is a compiled list of identified recordings, not a fully exhaustive discography.
Ndiye akuti mawa lino akutulutsaso ina 🔥
62
Happy birthday Colour Killer aka Crooksy, nako ku Police pano kwadzadza ma yoh. Komabe kwa ife ndi top fan uyu.
144
Koma inu a Malawi. Mwalandana Igwe zowona?😭
Kulandana Odogwu inu.
M’mene tayiveta nkhaniyo akuti zinali chonchi:
Ati anthu anyamukira limodzi atapangana kuti akakhala apartment imodzi ku Nigeria’ko. Ndiye m’modzi mwa anthuwo amadziwana ndi Oga kumeneko.
Kenako atafika, basi wapanga introduce kuti awa ndi anzanga aku Malawi. M’mene akutelo, Igwe aja awona chokhalira cha winayo, mtima osawupeza mpaka asaka number kwa Malawi ena.
Basitu, nayeso wathuyo walora, mpaka amuchotsako ku apartment ko ayamba kukhala limodzi kuhotelo. Ndiye yawo ija ma Nigeria yokonda kumatchitsa, anamusokera zoti amatchitse. Atulukira ku club weekend iyi atagwirana thako uku avala zomatcha.
Olandidwayo ati basi wanyanyala wachokako wabwerako zamunyasa. M’mene zikuwonekera, walandayu abwerako ndi forex yambiri chifukwa Oga amenewo si munthu wamba. Ali ndi thumba.
Izi tangova. Zitha kukhalanso zonama. Koma tapanga confirm kuti winayo wabwerakodi wanyanyalako.
12
4,950
Kodi muti zutani ku Nigeria? Zikuveka kuti a Malawi mwalandana mwamuna kumeneko. Nthawi yomweyi mwalandana kale Oga 🙌🏽
133
Zambian rapper Dizmo wagula ma car awiri pa tsiku limodzi, Range Rover Velar ndi Mercedes-Benz S400. Koma zoona zake, munthu ngati uyu angalime munda? Ine ndikukayika kwambiri!
Tiyamikire azathu anaboola ntambowa kupita kwa America, ndalama akupeza kumenekozo sakudya okha, akudya ndima followers awo omwe akuwapanga join pa live yawo 👏🏾
Mongokumbutsana uyu ndi Rayhan, akuchita kuonetsa kuti akudyapo bwino pa Khameri, inuso kadyakoni nzanu. Mongopanga Sign up pa Kick, kumupanga follow, then mupakuleko !
129































