Queen of Nibble Nibble retweeted
Ambirife nde chipanda chisomo cha mulungu bwezi tili makape kwambiri.
Line ya fuel pa nyambadwe Simso yazungulira Leroca kulowa nsewu wafumbi nkuzatulukira side inayi pa Total
Nde ena aombana pompo kufuna kulowelera, ntchito ilipo
56
😂ah iwe
Replying to @_Mzala
Koma she’s right . Why people do people go plain with people they don’t see long term.
1
65
I like your confidence
Just give @Dreamweave265 chance to be a main supplier! We can sort this within 30 days











