XVIII. retweeted
Utha kudabwa masiku akupita iwe ulibe chibwenzi. Osadziwa kuti your soulmate once saw you on your friend's status, anapempha nambala yako koma anamukaniza. Anamuwuza kuti ndiwe opanda khalidwe komanso wachisawawa.
XVIII. retweeted
Koma guys kungomugulila Mkazi mowa basi ikathele kuwaya? Brutal Fruit mutatu basi mpaka muvulane??🤣🤣🤣🤣
XVIII. retweeted
Ku Malawi kuno utaganiza zoti you will only be sexually active zinthu zako zikazayamba kukuyendera, utha kumwalira ukadali virgin.
XVIII. retweeted
I hate it when someone just starts apologizing right after kukulakwira chinachake. Like bro tandisiye Kaye ndikwiye bwinobwino, chindiphwele nde uzipepesa bwino.
XVIII. retweeted
I've noticed a pattern.
When you're taking too long to ask for their number, they'll say something like:
"mixeww kodi paja kuno kulibe ma sticker"
cholinga unene kuti "Tiye ku WhatsApp"😂🤣
XVIII. retweeted
Replying to @DonKhiva
Straight 🤝munthu sungatenga morale the rapper kumusiya pakhomo
XVIII. retweeted
Mafunyeta died at his peak 😭 he had so much to teach and show us, he was so unique, he brought his own sound and he went with it years later we still remember and want to copy his sounds because it was so unique and special
XVIII. retweeted
How is it my problem that I got a beautiful girl and yours has very questionable looks?
XVIII. retweeted
Musamasokoneze Kukhala Artist Ndi Kukhala Zokudya Zama Artist! Mwamva Aunt @Temwah265 ???
XVIII. retweeted
I'll vote for Thom Mpinganjira if this is true bro. The guy already has money. Office ija osazaikaso oshota kale . We learnt from Lazarus Chakwera 😎





















